Yesaya 18:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti Yehova watero kwa ine, Ine ndidzakhala cete, ndipo ndidzayang'ana mokhala cete, ndipo ndidzayang'ana mokhalamo Ine, monga kuwala kotentha kwa dzuwa, monga mtambo wa mame m'kutentha kwa masika.

Yesaya 18

Yesaya 18:1-7