Yesaya 18:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti masika asanafike, kutatha kuphuka ndi posanduka duwa mphesa yofuna kucha, iye adzadzombolera tinthambi ndi mphopo, ndi nthambi zotasa adzazicotsa ndi kuzisadza.

Yesaya 18

Yesaya 18:1-7