Yesaya 18:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Inunonseakukhala m'dziko lapansi, ndi inu akukhazikika pa dziko lapansi, potukulidwa cizindikiro pamwamba pa mapiri, mudzaona, ndi polizidwa lipenga mudzamva.

Yesaya 18

Yesaya 18:1-7