Yesaya 17:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Katundu wa Damasiko. Taonani, Damasiko wacotsedwa usakhalenso mudzi, ndimo udzangokhala muunda wopasudwa.

Yesaya 17

Yesaya 17:1-6