Yesaya 16:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma tsopano Yehova wanena, nati, Zisanapite zaka zitatu monga zaka za wolembedwa nchito, ulemerero wa Moabu udzakhala wonyozeka, ndi khamu lalikuru lace, ndi otsala adzakhala ang'ongong'ono ndi acabe.

Yesaya 16

Yesaya 16:9-14