Yeremiya 6:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Yehova atero, Taona, mtundu wa anthu ucokera kumpoto; ndi mtundu waukuru adzaukitsidwa ku malekezero a dziko lapansi.

Yeremiya 6

Yeremiya 6:18-24