Yeremiya 6:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Agwira uta ndi nthungo; ali ankharwe, alibe cifundo; mau ao aphokosera ngati nyanja, akwera pa akavalo; aguba monga anthu ofuna kumenyana nkhondo ndi iwe, mwana wamkazi wa Ziyoni.

Yeremiya 6

Yeremiya 6:14-30