Yeremiya 6:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace atero Yehova, Taona, ndidzaikira anthuwa zopunthwitsa; ndipo atate ndi ana adzakhumudwa nazo pamodzi; munthu ndi mnzace adzatayika.

Yeremiya 6

Yeremiya 6:17-24