Yeremiya 51:47 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace, taonani, masiku alinkudza, amene ndidzaweruza mafano osemasema a Babulo, ndipo dziko lace lonse lidzakhala ndi manyazi; ndipo ophedwa ace onse adzagwa pakati pace.

Yeremiya 51

Yeremiya 51:39-54