Oweruza 7:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yehova anati kwa Gideoni. Anthu ali ndi iwe andicurukira kuti ndipereke Midyani m'dzanja lao; angadzitame Israyeli pa Ine, ndi kuti, Dzanja la ine mwini landipulumutsa.

Oweruza 7

Oweruza 7:1-12