Oweruza 19:30 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kunali kuti onse amene anaciona anati, Sicinacitika, inde sicinaoneka cotere ciyambire tsiku lokwera ana a Israyeli kuturuka m'dziko la Aigupto mpaka lero lino; lingiriranipo, mupangane nzeru, nimunene.

Oweruza 19

Oweruza 19:29-30