Oweruza 19:29 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pofika iye kunyumba kwace, anatenga mpeni, nagwira mkazi wace wamng'onoyo namgawa ciwalo ciwalo magawo khumi ndi awiri, namtumiza ku mame onse a Israyeli.

Oweruza 19

Oweruza 19:19-30