Oweruza 11:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma Sihoni sanakhulupirira Israyeli kuti apitire pakati pa malire ace; koma Sihoni anamemeza anthu ace onse, namanga misasa ku Yahazi, nathira nkhondo Israyeli.

Oweruza 11

Oweruza 11:11-30