Oweruza 11:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Israyeli anatuma mithenga kwa Sihoni mfumu ya Aamori, mfumu ya ku Hesiboni; nanena naye Israyeli, Tikupemphani tipitire pakati pa dziko lanu, kumka kwathu.

Oweruza 11

Oweruza 11:11-24