Nyimbo 1:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndiuze, iwe amene moyo wanga ukukonda,Umaweta kuti gulu lako?Umaligonetsa kuti pakati pa usana?Pakuti ndikhalirenji ngati wosoceraPambali pa magulu a anzako?

Nyimbo 1

Nyimbo 1:6-13