Nahumu 1:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mapiri agwedezeka cifukwa ca Iye, ndi zitunda zisungunuka; ndi dziko lapansi likwezeka pamaso pace, ndi maiko ndi onse okhala m'mwemo.

Nahumu 1

Nahumu 1:1-14