Nahumu 1:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Adzaima ndani pa kulunda kwace? ndipo adzakhalitsa ndani pa mkwiyo wace wotentha? ukali wace utsanulidwa ngati moto, ndi matanthwe asweka ndi Iye.

Nahumu 1

Nahumu 1:2-12