Nahumu 1:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Adzudzula nyanja, naiphwetsa, naumitsa mitsinje yonse; Basana ndi Karimeli afota, ndi duwa la ku Lebano linyala.

Nahumu 1

Nahumu 1:1-9