Mika 4:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndipo wotsimphinayo ndidzamuyesa wotsala, ndi iye wotayidwa kutali mtundu wamphamvu; ndipo Yehova adzakhala mfumu yao m'phiri la Ziyoni kuyambira pamenepo kufikira kosatha.

Mika 4

Mika 4:1-11