Mika 4:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo iwe, nsanja ya nkhosa, citunda ca mwana wamkazi wa Ziyoni, udzafikira iwe, inde udzafika ulamuliro wakale, ufumu wa mwana wamkazi wa Yerusalemu.

Mika 4

Mika 4:1-13