Mika 4:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Tsiku ilo, ati Yehova, ndidzamemeza wakutsimphinayo, ndi kusonkhanitsa wopitikitsidwayo, ndi iye amene ndinamsautsa;

Mika 4

Mika 4:1-8