Mateyu 7:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ambiri adzati kwa Ine tsiku lomwelo, Ambuye, Ambuye, kodi sitinanenera mau m'dzina lanu, ndi m'dzina lanunso kuturutsa mizimu yoipa, ndi kucita m'dzina lanunso zamphamvu zambiri?

Mateyu 7

Mateyu 7:18-26