Mateyu 7:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pamenepo ndidzafukulira iwo, Sindinakudziwani inu nthawi zonse; cokani kwa Ine, inu akucita kusayeruzika.

Mateyu 7

Mateyu 7:18-24