Mateyu 7:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Si yense wakunena kwa Ine, Ambuye, Ambuye, adzalowa mu Ufumu wa Kumwamba; koma wakucitayo cifuniro ca Atate wanga wa Kumwamba.

Mateyu 7

Mateyu 7:13-25