Mateyu 4:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Kuyambira pamenepo Yesu anayamba kulalikira, ndi kunena, Tembenukani mitima, pakuti Ufumu wa Kumwamba wayandikira.

Mateyu 4

Mateyu 4:8-20