Anthu akukhala mumdimaAdaona kuwala kwakukuru,Ndi kwa iwo okhala m'malo mthunzi wa imfa,Kuwala kunaturukira iwo.