Mateyu 4:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pamene Yesu analikuyenda m'mbali mwa nyanja ya Galileya, anaona abale awiri, Simoni wonenedwa Petro, ndi Andreya, mbale wace, analikuponya psasa m'nyanja; popeza anali asodzi a nsomba.

Mateyu 4

Mateyu 4:14-23