Mateyu 25:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mbuye wace anati kwa iye, Cabwino, kapolo iwe wabwino ndi wokhulupirika; unali wokhulupirika pa zinthu zazing'ono, ndidzakhazika iwe pa zinthu zambiri; Iowa iwe m'cikondwero ca mbuye wako.

Mateyu 25

Mateyu 25:16-26