Mateyu 25:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo wa ndalama ziwiriyo anadzanso, nati, Mbuye, munandipatsa ine ndalama ziwiri; onani, ndapindulapo ndalama zina ziwiri.

Mateyu 25

Mateyu 25:18-28