Mateyu 25:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo uyonso amene analandira ndalama imodzi, anadza, nati, Mbuye, ndinakudziwani inu kuti ndinu munthu wouma mtima, wakututa kumene simunafesa, ndi wakusonkhanitsa kumene simunawaza;

Mateyu 25

Mateyu 25:20-27