Mateyu 16:27 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti Mwana wa munthu adzabwera mu ulemerero wa Atate wace, pamodzi ndi angelo ace; ndipo pomwepo Iye adzabwezera kwa anthu onse monga macitidwe ao.

Mateyu 16

Mateyu 16:18-28