Mateyu 16:28 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Indetu ndinena kwa inu, kuti alipo ena a iwo aima pane sadzalawa ndithu imfa, kufikira adzaona Mwana wa munthu atadza mu ufumu wace.

Mateyu 16

Mateyu 16:20-28