Mateyu 16:26 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti munthu adzapindulanji, akalandira dziko lonse, nataya moyo wace? kapena munthu adzaperekanji cosintha ndi moyo wace?

Mateyu 16

Mateyu 16:25-28