Mateyu 12:31 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace ndinena kwa inu, Macimo onse, ndi zonena zonse zamwano, zidzakhululukidwa kwa anthu; koma camwano ca pa Mzimu Woyera sicidzakhululukidwa.

Mateyu 12

Mateyu 12:22-40