Mateyu 12:32 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo amene ali yense anganenere Mwana wa munthu zoipa, adzakhululukidwa; koma amene ali yense anganenere Mzimu Woyera zoipa sadzakhululukidwa nthawi yino kapena irinkudzayo.

Mateyu 12

Mateyu 12:27-35