Marko 9:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Iye anawayankha nanena, Mbadwo wosakhulupirira inu, ndidzakhala ndi inu kufikira liti? ndidzakulekererani nthawi yanji? Mudze naye kwa Ine.

Marko 9

Marko 9:13-21