Marko 9:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anadza naye kwa Iye; ndipo pakumuona, pomwepo mzimuwo unamng'amba koopsya; ndipo anagwa pansi nabvimbvinika ndi kucita thobvu.

Marko 9

Marko 9:17-29