Marko 9:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndipo ponse pamene umgwira, umgwetsa; ndipo acita thobvu, nakukuta mano, nanyololoka; ndipo ndinalankhula nao ophunzira anu kuti auturutse; koma sanakhoza.

Marko 9

Marko 9:8-21