Maliro 2:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Wathifula uta wace ngati mdani, waima ndi dzanja lace lamanja ngati mmaliwongo;Wapha onse okondweretsa maso;Watsanulira ukali wace ngati moto pa hema wa mwana wamkazi wa Ziyoni.

Maliro 2

Maliro 2:3-5