Maliro 2:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pokwiya moopsya walikha nyanga zonse za Israyeli;Wabweza m'mbuyo dzanja lace lamanja pamaso pa adaniwo,Natentha Yakobo ngati moto wamalawi wonyambita mozungulira.

Maliro 2

Maliro 2:1-12