Maliro 2:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Yehova wasanduka mdani, wameza Israyeli;Wameza zinyumba zace zonse, wapasula malinga ace;Nacurukitsira mwana wamkazi wa Yuda maliro ndi cibumo.

Maliro 2

Maliro 2:1-9