Macitidwe 25:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma Paulo anati, ndirikuimirira pa mpando waciweruziro wa Kaisara, pompano ndiyenera kuweruzidwa ine; Ayuda sindinawacitira-kanthu koipa, monga mudziwanso nokha bwino.

Macitidwe 25

Macitidwe 25:2-12