Macitidwe 25:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo ngati ndiri wocita zoipa, ngati ndacita kanthu kakuyenera imfa, sindikana kufa; koma ngati zinthuzi awa andinenera nazo ziri zacabe, palibe mmodzi akhoza kundipereka kwa iwo. Nditurukira kwa Kaisara.

Macitidwe 25

Macitidwe 25:7-19