Macitidwe 25:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Kama Festo pofuna kuyesedwa wacisomo ndi Ayuda, anayankha kwa Paulo, nati, Kodi ufuna kukwera kunka ku Yerusalemu, ndi kuweruzidwa ndi ine pomwepo kunena za zinthu izi?

Macitidwe 25

Macitidwe 25:1-18