Luka 9:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo iye ananena kwa onse, Ngati munthu afuna kudza pambuyo panga, adzikanize yekha, nanyamule mtanda wace tsiku ndi tsiku, nanditsate Ine.

Luka 9

Luka 9:14-32