Luka 9:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakutiamene ali yense akafuna kupulumutsa moyo wace, iye adzautaya; koma amene ali yense akataya moyo wace cifukwa ca Ine, iye adzaupulumutsa uwu.

Luka 9

Luka 9:17-25