Luka 9:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

nati, Kuyenera kuti Mwana wa munthu amve zowawa zambiri, ndi kukanidwa ndi akuru, ndi ansembe akuru, ndi alembi, ndi kuphedwa, ndi kuuka tsiku lacitatu.

Luka 9

Luka 9:21-31