Levitiko 20:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Munthu akacita cigololo ndi mkazi wa mwini, popeza wacita cigololo ndi mkazi wa mnansi wace, awaphe nditho, mwamuna ndi mkazi onse awiri.

Levitiko 20

Levitiko 20:1-13