Levitiko 20:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti ali yense wakutemberera atate wace kapena mai wace azimupha ndithu; watemberera atate wace kapena mai wace; mwazi wace ukhale pamutu pace.

Levitiko 20

Levitiko 20:1-18