Levitiko 20:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Munthu akagona naye mkazi wa atate wace, wabvula atate wace; awaphe ndithu onse awiri; mwazi wao ukhale pamtu pao.

Levitiko 20

Levitiko 20:4-18